Kadigong (Remix)-文本歌词

Kadigong (Remix)-文本歌词

Sho Madjozi&Tiwa Savage&Zeze Kingston&Gemini Major&Ntando yamahlubi&Tee Jay
发行日期:

Moni moni moni

Kuyilowa ndi mutu

Ndasiya mudothi

Mayazi maya mayazi

Gwira malaya nane ndi ilowe basi

Mayazi mayazi mayazi

Kuyilowa ndi mutu mopanda manyazi

Maya mayazi mayazi

Nkhani yamanyado ilbe n’khala pakati

Mayazi mayazi mayazi

Okudya ndalama samatcheka balansi

Vina

Tchola

Tshika

Kadi gong

Sinali plani kuti ndikukonde

(Koma)

watshekemela ngati ndiwe combe

(Ona)

Watseleekeza ma guy wonse

odi ndi ka pote

Tizitchiiilla tiKhale Pa easy

Ndili ndi mandede ngati Iani lizzi

Ndimakoonda njonda zachimidzi

A/khale wauleemu opanda utchissi

Tenga u/moodzi tinyowe kukhosi

(Nane ndima/nyowa uka/kamba zaku\\khosi

Ndikutengele ku/Jhoni u/kawone tshotshi (jozi)

U/kazipeza /ndi achina Sho madJozi konkoo

Ndi/libe phuma ndine nkazi wodeekha

Koma ndi Kabwella undi/vulile wekha

.Mfana woteentha ta/ziiyiteleka

ku/mayi chakulila ndika/mayi peleka

Intercontinental baddie gbemidebe

You talking shi like you constipated

You talking money like you gbemidebe

Loudaaaa

Wena sowa

Ita lawa

Redi redi for the baller

Body body body badder x2

Vina

Tchola

Tshika

Kadi gong

Eyo tiyeni, Tiyeni Tiyeni Tiyeni eish

Ati Mayazi Mayazi Mayazi

Izi zolondana mapazizi

Ponda apa Mpondepo

Game yamagazi

Ati Mayazi Mayazi Mayazi

Izi zolondana mapazizi

Ponda apa Mpondepo?

Game yamagazi

Ndamuuza zochita

Kenako waganiza zopita eish

Ati tiyeni kuden kwanu

Pomaliza undipatsa 2 mita

Eh! Ndamuuza zochita

Kenako waganiza zopita

Ati tiyeni kuden kwanu

Pomaliza undipatsa 2 mita eish!

(Kwaola, Kwaola)

(Kwaola, Kwaola)

Eyo tiyeni, Tiyeni tiyeni tiyeni eish!

Vina

Tchola

Tshika

Kadi gong

Mkazi wakunja khalidwe lachimalawi

Ndipanga naye chani fukwa ndine mphawi

Nyumba yakwawo yaku mayadi

Makolo akachoka timapanga party

Chikondi cha season ngati mtengo wa mango

Koma ndatopa nane ndikhale wako

Uzi ndigwira gwira ngati kupanga chipako

Polama pango’no undigwiritse thako

Ndikukwatile kapena tipange chinkhoswe

Olo ndidzidya mwa chinsinsi ngati khoswe

Dona ya ulemu Ndipo alibe chipongwe

Ndimupatse mimba kuti akhale pakhonde

Wabwera ndi Bola odi ndikapote

Tikawone Nyanja Ng’ona ku liwonde

Kukunyaditsa kuti akuwone

A Nsanje kaduka onse aku zonde

Wena sowa

Ita lawa

Redi redi for the baller

Body body body badder

Okayyyy

Vina

Tchola

Tshika

Kadi gong